Levitiko 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Mkazi akatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira akamasamba.+ Levitiko 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Ngati mkazi akukha ndipo zimene akukhazo ndi magazi,+ azikhala masiku 7 ali wodetsedwa+ chifukwa cha kusamba+ kwakeko, ndipo aliyense womukhudza azikhala wodetsedwa kufikira madzulo. Levitiko 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno pa tsiku la 8 azitenga njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda, ndi kubwera nawo kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako.+ Levitiko 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Usayandikire mkazi kuti um’vule+ pamene ali wodetsedwa chifukwa cha kusamba+ kwake.
2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Mkazi akatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira akamasamba.+
19 “‘Ngati mkazi akukha ndipo zimene akukhazo ndi magazi,+ azikhala masiku 7 ali wodetsedwa+ chifukwa cha kusamba+ kwakeko, ndipo aliyense womukhudza azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.
29 Ndiyeno pa tsiku la 8 azitenga njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda, ndi kubwera nawo kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako.+