-
2 Samueli 14:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndiyeno mfumu inamufunsa kuti: “Kodi Yowabu+ ndi amene wakutuma?”+ Pamenepo mkaziyo anayankha kuti: “Pali moyo wanu+ mbuyanga mfumu, palibe munthu angapatukire kudzanja lamanja kapena lamanzere pa zonse zimene inu mbuyanga mfumu mwanena. Mtumiki wanu Yowabu ndi amene wandituma ndi kundiuza zonse zimene ndalankhula nanu.+
-