Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Uziopa Yehova Mulungu wako+ ndi kum’tumikira,+ ndipo uzilumbira pa dzina lake.+

  • Yeremiya 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+

  • Yeremiya 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Ndiyeno anthu a mitundu ina akadzaphunzira njira za anthu anga ndi kulumbira m’dzina langa+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’ monga mmene iwo anaphunzitsira anthu anga kulumbira m’dzina la Baala,+ anthu a mitundu inawo adzakhazikika pakati pa anthu anga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena