Genesis 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako, malowo anawatcha Beteli.+ Koma dzina lakale la mzindawo linali Luzi.+ 1 Mafumu 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno chifaniziro cha ng’ombe chimodzi anakachiika ku Beteli,+ china anakachiika ku Dani.+ 1 Mafumu 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano panali munthu+ wa Mulungu amene anatumidwa+ ndi Yehova kuchokera ku Yuda kupita ku Beteli. Kumeneko iye anapeza Yerobowamu ataimirira pambali pa guwa lansembe+ kuti afukize nsembe yautsi.+ 2 Mafumu 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Elisa ananyamuka kupita ku Beteli.+ Akuyenda kukwezeka chitunda, anyamata ena+ amene anachokera mumzinda anayamba kumunyoza mokuwa+ kuti: “Choka kuno wadazi iwe!+ Choka kuno wadazi iwe!”
13 Tsopano panali munthu+ wa Mulungu amene anatumidwa+ ndi Yehova kuchokera ku Yuda kupita ku Beteli. Kumeneko iye anapeza Yerobowamu ataimirira pambali pa guwa lansembe+ kuti afukize nsembe yautsi.+
23 Kenako Elisa ananyamuka kupita ku Beteli.+ Akuyenda kukwezeka chitunda, anyamata ena+ amene anachokera mumzinda anayamba kumunyoza mokuwa+ kuti: “Choka kuno wadazi iwe!+ Choka kuno wadazi iwe!”