1 Samueli 17:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Sauli ataona Davide akupita kukakumana ndi Mfilisiti uja, anafunsa Abineri,+ mkulu wa asilikali, kuti: “Kodi ameneyu ndi mwana+ wa ndani,+ Abineri?” Poyankha Abineri anati: “Ndikulumbira pali moyo wanu mfumu, ine sindikudziwa ngakhale pang’ono!” 2 Mafumu 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo mayi wa mwanayo anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo+ ndiponso pali moyo wanu+ sindikusiyani.”+ Choncho Elisa ananyamuka n’kupita pamodzi ndi mayiyo.
55 Sauli ataona Davide akupita kukakumana ndi Mfilisiti uja, anafunsa Abineri,+ mkulu wa asilikali, kuti: “Kodi ameneyu ndi mwana+ wa ndani,+ Abineri?” Poyankha Abineri anati: “Ndikulumbira pali moyo wanu mfumu, ine sindikudziwa ngakhale pang’ono!”
30 Pamenepo mayi wa mwanayo anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo+ ndiponso pali moyo wanu+ sindikusiyani.”+ Choncho Elisa ananyamuka n’kupita pamodzi ndi mayiyo.