1 Samueli 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atamva zimenezi, Sauli anatuma mithenga kwa Jese, kuti: “Nditumizire mwana wako Davide amene akuweta nkhosa.”+ 1 Samueli 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Davide anapita kwa Sauli ndipo anali kum’tumikira.+ Sauli anam’konda kwambiri Davide, moti anakhala womunyamulira zida zake.+
19 Atamva zimenezi, Sauli anatuma mithenga kwa Jese, kuti: “Nditumizire mwana wako Davide amene akuweta nkhosa.”+
21 Choncho Davide anapita kwa Sauli ndipo anali kum’tumikira.+ Sauli anam’konda kwambiri Davide, moti anakhala womunyamulira zida zake.+