1 Samueli 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo Hana anati: “Pepani mbuyanga! Pali moyo wanu+ mbuyanga, ine ndine mkazi amene ndinaima ndi inu pamalo ano n’kupemphera kwa Yehova.+ 2 Mafumu 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano Eliya anauza Elisa kuti: “Khala apa Elisa, pakuti ine Yehova wandituma ku Yeriko.”+ Koma Elisa anayankha kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo ndiponso pali moyo wanu, sindikusiyani.” Choncho iwo anafika ku Yeriko.
26 Pamenepo Hana anati: “Pepani mbuyanga! Pali moyo wanu+ mbuyanga, ine ndine mkazi amene ndinaima ndi inu pamalo ano n’kupemphera kwa Yehova.+
4 Tsopano Eliya anauza Elisa kuti: “Khala apa Elisa, pakuti ine Yehova wandituma ku Yeriko.”+ Koma Elisa anayankha kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo ndiponso pali moyo wanu, sindikusiyani.” Choncho iwo anafika ku Yeriko.