Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 141:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+

      Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+

      Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+

      Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+

  • Miyambo 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira.

  • Miyambo 25:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera, amakhala ngati ndolo* yagolide, ndiponso ngati chokongoletsera chagolide wapadera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena