Genesis 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Timvereni mbuyathu.+ Inu ndinu mtsogoleri woikidwa ndi Mulungu.+ Sankhani manda abwino koposa pa manda amene tili nawo kuti muikemo malemuwo.+ Palibe aliyense wa ife amene angakanize manda ake kuti muikemo malemuwo.”+ Aroma 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo.
6 “Timvereni mbuyathu.+ Inu ndinu mtsogoleri woikidwa ndi Mulungu.+ Sankhani manda abwino koposa pa manda amene tili nawo kuti muikemo malemuwo.+ Palibe aliyense wa ife amene angakanize manda ake kuti muikemo malemuwo.”+
10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo.