Yesaya 53:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Manda ake adzakhala limodzi ndi a anthu oipa,+ ndipo adzakhala limodzi ndi anthu olemera pa imfa yake,+ ngakhale kuti iye sanachite zachiwawa zilizonse+ ndipo m’kamwa mwake munalibe chinyengo.+ Yohane 19:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Tsopano kumalo kumene anamupachikirako kunali munda. M’munda umenewo munali manda achikumbutso+ atsopano, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.
9 Manda ake adzakhala limodzi ndi a anthu oipa,+ ndipo adzakhala limodzi ndi anthu olemera pa imfa yake,+ ngakhale kuti iye sanachite zachiwawa zilizonse+ ndipo m’kamwa mwake munalibe chinyengo.+
41 Tsopano kumalo kumene anamupachikirako kunali munda. M’munda umenewo munali manda achikumbutso+ atsopano, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.