Mateyu 27:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Tsopano madzulo, munthu wina wachuma wa ku Arimateya, wotchedwa Yosefe, amenenso anakhala wophunzira wa Yesu,+ Maliko 15:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+ Yohane 19:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Tsopano kumalo kumene anamupachikirako kunali munda. M’munda umenewo munali manda achikumbutso+ atsopano, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.
57 Tsopano madzulo, munthu wina wachuma wa ku Arimateya, wotchedwa Yosefe, amenenso anakhala wophunzira wa Yesu,+
46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+
41 Tsopano kumalo kumene anamupachikirako kunali munda. M’munda umenewo munali manda achikumbutso+ atsopano, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.