Mateyu 27:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 ndipo anakauika m’manda ake achikumbutso atsopano,+ amene anawasema m’thanthwe. Kenako anagubuduza chimwala chachikulu ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo, n’kuchoka.+ Luka 23:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Choncho anautsitsa+ ndi kuukulunga munsalu yabwino kwambiri, kenako anakauika m’manda+ ogobedwa muthanthwe, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.+ Yohane 19:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu n’kuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ malinga ndi mwambo umene Ayuda anali kutsatira poika maliro.
60 ndipo anakauika m’manda ake achikumbutso atsopano,+ amene anawasema m’thanthwe. Kenako anagubuduza chimwala chachikulu ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo, n’kuchoka.+
53 Choncho anautsitsa+ ndi kuukulunga munsalu yabwino kwambiri, kenako anakauika m’manda+ ogobedwa muthanthwe, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.+
40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu n’kuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ malinga ndi mwambo umene Ayuda anali kutsatira poika maliro.