Maliko 15:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+ Luka 23:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Choncho anautsitsa+ ndi kuukulunga munsalu yabwino kwambiri, kenako anakauika m’manda+ ogobedwa muthanthwe, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.+ Yohane 19:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Tsopano kumalo kumene anamupachikirako kunali munda. M’munda umenewo munali manda achikumbutso+ atsopano, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.
46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+
53 Choncho anautsitsa+ ndi kuukulunga munsalu yabwino kwambiri, kenako anakauika m’manda+ ogobedwa muthanthwe, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.+
41 Tsopano kumalo kumene anamupachikirako kunali munda. M’munda umenewo munali manda achikumbutso+ atsopano, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.