Machitidwe 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno iwo atakwaniritsa zinthu zonse zolembedwa zonena za iye,+ anamutsitsa pamtengo+ ndi kumuika m’manda achikumbutso.+
29 Ndiyeno iwo atakwaniritsa zinthu zonse zolembedwa zonena za iye,+ anamutsitsa pamtengo+ ndi kumuika m’manda achikumbutso.+