Luka 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Tamverani! Tsopano tikupita ku Yerusalemu, ndipo zonse zimene zinalembedwa ndi aneneri,+ zokhudza Mwana wa munthu zikakwaniritsidwa.+ Yohane 19:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kwenikweni izi zinachitika kuti lemba likwaniritsidwe, pamene linati: “Sadzathyola fupa lake ndi limodzi lomwe.”+
31 Kenako anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Tamverani! Tsopano tikupita ku Yerusalemu, ndipo zonse zimene zinalembedwa ndi aneneri,+ zokhudza Mwana wa munthu zikakwaniritsidwa.+
36 Kwenikweni izi zinachitika kuti lemba likwaniritsidwe, pamene linati: “Sadzathyola fupa lake ndi limodzi lomwe.”+