Mateyu 27:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 ndipo anakauika m’manda ake achikumbutso atsopano,+ amene anawasema m’thanthwe. Kenako anagubuduza chimwala chachikulu ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo, n’kuchoka.+
60 ndipo anakauika m’manda ake achikumbutso atsopano,+ amene anawasema m’thanthwe. Kenako anagubuduza chimwala chachikulu ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo, n’kuchoka.+