Yesaya 53:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Manda ake adzakhala limodzi ndi a anthu oipa,+ ndipo adzakhala limodzi ndi anthu olemera pa imfa yake,+ ngakhale kuti iye sanachite zachiwawa zilizonse+ ndipo m’kamwa mwake munalibe chinyengo.+ Machitidwe 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno iwo atakwaniritsa zinthu zonse zolembedwa zonena za iye,+ anamutsitsa pamtengo+ ndi kumuika m’manda achikumbutso.+
9 Manda ake adzakhala limodzi ndi a anthu oipa,+ ndipo adzakhala limodzi ndi anthu olemera pa imfa yake,+ ngakhale kuti iye sanachite zachiwawa zilizonse+ ndipo m’kamwa mwake munalibe chinyengo.+
29 Ndiyeno iwo atakwaniritsa zinthu zonse zolembedwa zonena za iye,+ anamutsitsa pamtengo+ ndi kumuika m’manda achikumbutso.+