Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.

  • 1 Samueli 26:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tsopano mbuyanga mfumu, mvetserani mawu a mtumiki wanu: Ngati Yehova ndiye wakutumani kuti mundiukire, iye alandire nsembe yanga yambewu.+ Koma ngati ndi ana a anthu,+ atembereredwe pamaso pa Yehova,+ chifukwa andipitikitsa ndi kundichotsa lero kuti ndisamve kuti ndili pafupi ndi cholowa cha Yehova,+ mwa kundiuza kuti, ‘Pita ukatumikire milungu ina!’+

  • Salimo 101:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Aliyense wonenera mnzake miseche,+

      Ndimamukhalitsa chete.+

      Sindingathe kupirira zochita za+

      Aliyense wodzikweza ndi wamtima wonyada.+

  • Miyambo 16:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kazitape amangokhalira kuyambitsa mikangano,+ ndipo wonenera anzake zoipa amalekanitsa mabwenzi apamtima.+

  • Miyambo 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Wochita zoipa amamvetsera mlomo wolankhula zopweteka ena.+ Wonama amamvetsera lilime loyambitsa mavuto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena