Levitiko 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Mukamapereka nsembe yachiyanjano kwa Yehova,+ muziipereka m’njira yakuti Mulungu akuyanjeni.+ 2 Samueli 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamenepo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliriwo anauthetsa mu Isiraeli.
25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamenepo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliriwo anauthetsa mu Isiraeli.