Levitiko 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mukamapereka nsembe yamgwirizano kwa Yehova,+ muziipereka mʼnjira yakuti Mulungu asangalale nanu.+