Levitiko 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Mukamapereka nsembe yachiyanjano kwa Yehova,+ muziipereka m’njira yakuti Mulungu akuyanjeni.+