Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano njoka+ inali yochenjera kwambiri+ kuposa nyama zonse zakutchire zimene Yehova Mulungu anapanga.+ Ndipo njokayo inafunsa mkaziyo+ kuti: “Eti n’zoona kuti Mulungu anati musadye zipatso za mtengo uliwonse wa m’mundamu?”+

  • 1 Samueli 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno Davide anauza Sauli kuti: “N’chifukwa chiyani mukumvera mawu a anthu,+ akuti, ‘Davide akufuna kukuvulazani’?

  • Miyambo 18:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mawu a munthu wonenera ena zoipa ali ngati zinthu zofunika kuzimeza msangamsanga,+ zimene zimatsikira mkatikati mwa mimba.+

  • Aroma 16:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+

  • 2 Akorinto 12:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndikuopa kuti mwinamwake ndikadzafika,+ sindidzakupezani mmene ndikanafunira. Kwa inunso sindidzakhala mmene mukanafunira. M’malomwake, ndidzapeza ndewu, nsanje,+ kukwiyitsana, mikangano, miseche, manong’onong’o, kudzitukumula, ndi zisokonezo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena