Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndithu ndikanakonda kuti anthu amene akuona kuti ifeyo timachita zinthu motsatira maganizo a dzikoli,* asinthe maganizo awo, kuti ndikadzabwera kumeneko ndisadzachite zinthu zazikulu zotsutsana nawo.+

  • 2 Akorinto 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ngakhale kuti panopa ndili kutali ndi inu, koma muone mawu angawa ngati kuti ndili limodzi nanu kachiwiri. Choncho, monga mmene ndinachitira kale, ndikuchenjeza anthu amene anachimwa, komanso ena onse, kuti ndikadzabweranso kumeneko sindidzalekerera munthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena