Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mulungu akhale mboni+ pa moyo wanga kuti chifukwa chimene sindinabwererebe ku Korintoko n’chakuti sindinafune kuti ndidzawonjezere chisoni chanu.+

  • 2 Akorinto 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndithu ndikanakonda kuti anthu amene akuona kuti ifeyo timachita zinthu motsatira maganizo a dzikoli,* asinthe maganizo awo, kuti ndikadzabwera kumeneko ndisadzachite zinthu zazikulu zotsutsana nawo.+

  • 2 Akorinto 12:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mwina ndikadzabweranso, Mulungu wanga adzandichititsa manyazi pakati panu. Ndipo mwina ndidzalirira anthu ambiri amene anachimwa+ koma sanalape pa zonyansa zawo, dama*+ lawo, ndi khalidwe lawo lotayirira+ limene akhala akuchita.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena