1 Akorinto 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mbiri yamvekatu kuti pakuchitika dama*+ pakati panu, ndipo dama lake ndi loti ngakhale anthu a mitundu ina sachita. Akuti mwamuna wina watengana ndi mkazi wa bambo ake.+ 2 Akorinto 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti ngati ndingakuchititseni kumva chisoni,+ adzandisangalatsa ndani kupatulapo amene ndawachititsa kumva chisoniwo?
5 Mbiri yamvekatu kuti pakuchitika dama*+ pakati panu, ndipo dama lake ndi loti ngakhale anthu a mitundu ina sachita. Akuti mwamuna wina watengana ndi mkazi wa bambo ake.+
2 Pakuti ngati ndingakuchititseni kumva chisoni,+ adzandisangalatsa ndani kupatulapo amene ndawachititsa kumva chisoniwo?