Genesis 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Isiraeli atamanga msasa+ m’dziko limenelo, Rubeni anagona ndi Biliha mkazi wamng’ono* wa bambo ake, ndipo Isiraeli anamva zimene zinachitikazo.+ Yakobo anali ndi ana aamuna 12. Levitiko 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Usavule mkazi wa bambo ako,+ chifukwa kumeneko n’kuvula bambo ako. Deuteronomo 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Pasapezeke mwamuna aliyense wotenga mkazi wa bambo ake kuopera kuti angavule bambo akewo.+
22 Isiraeli atamanga msasa+ m’dziko limenelo, Rubeni anagona ndi Biliha mkazi wamng’ono* wa bambo ake, ndipo Isiraeli anamva zimene zinachitikazo.+ Yakobo anali ndi ana aamuna 12.