Aefeso 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dama*+ ndi chonyansa chamtundu uliwonse kapena umbombo+ zisatchulidwe n’komwe pakati panu,+ monga mmene anthu oyera amayenera kuchitira.+
3 Dama*+ ndi chonyansa chamtundu uliwonse kapena umbombo+ zisatchulidwe n’komwe pakati panu,+ monga mmene anthu oyera amayenera kuchitira.+