2 Akorinto 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwina ndikadzabweranso, Mulungu wanga adzandichititsa manyazi pakati panu. Ndipo mwina ndidzalirira anthu ambiri amene anachimwa+ koma sanalape pa zonyansa zawo, dama*+ lawo, ndi khalidwe lawo lotayirira+ limene akhala akuchita.
21 Mwina ndikadzabweranso, Mulungu wanga adzandichititsa manyazi pakati panu. Ndipo mwina ndidzalirira anthu ambiri amene anachimwa+ koma sanalape pa zonyansa zawo, dama*+ lawo, ndi khalidwe lawo lotayirira+ limene akhala akuchita.