1 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+ 1 Akorinto 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chakudya ndi cha mimba, ndipo mimba ndi ya chakudya,+ koma Mulungu adzawononga mimba ndi chakudya chomwe.+ Choncho thupi silochitira dama koma ndi la Ambuye,+ ndipo Ambuye ndiye mwini thupi.+
9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+
13 Chakudya ndi cha mimba, ndipo mimba ndi ya chakudya,+ koma Mulungu adzawononga mimba ndi chakudya chomwe.+ Choncho thupi silochitira dama koma ndi la Ambuye,+ ndipo Ambuye ndiye mwini thupi.+