Aroma 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ndi moyo wanga wonse polalikira uthenga wabwino wonena za Mwana wake, ndiye mboni yanga+ ya mmene ndimakutchulirani m’mapemphero anga nthawi zonse.+ Afilipi 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu ndiye mboni yanga kuti ndikufunitsitsa nditakuonani nonsenu. Ndikufunitsitsa nditakuonani ndi chikondi chachikulu+ ngati chimene Khristu Yesu ali nacho.
9 Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ndi moyo wanga wonse polalikira uthenga wabwino wonena za Mwana wake, ndiye mboni yanga+ ya mmene ndimakutchulirani m’mapemphero anga nthawi zonse.+
8 Mulungu ndiye mboni yanga kuti ndikufunitsitsa nditakuonani nonsenu. Ndikufunitsitsa nditakuonani ndi chikondi chachikulu+ ngati chimene Khristu Yesu ali nacho.