Akolose 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero monga ochita kusankhidwa ndi Mulungu,+ oyera ndi okondedwa, valani chifundo+ chachikulu, kukoma mtima, kudzichepetsa,+ kufatsa,+ ndi kuleza mtima.+
12 Chotero monga ochita kusankhidwa ndi Mulungu,+ oyera ndi okondedwa, valani chifundo+ chachikulu, kukoma mtima, kudzichepetsa,+ kufatsa,+ ndi kuleza mtima.+