Tito 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Asamanenere zoipa munthu aliyense, ndipo asakhale aukali.+ Koma akhale ololera,+ ndi ofatsa kwa anthu onse.+ 1 Petulo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma kukhale kwa munthu wobisika+ wamumtima, atavala zovala zosawonongeka,+ ndizo mzimu wabata ndi wofatsa+ umene uli wamtengo wapatali pamaso pa Mulungu.
2 Asamanenere zoipa munthu aliyense, ndipo asakhale aukali.+ Koma akhale ololera,+ ndi ofatsa kwa anthu onse.+
4 Koma kukhale kwa munthu wobisika+ wamumtima, atavala zovala zosawonongeka,+ ndizo mzimu wabata ndi wofatsa+ umene uli wamtengo wapatali pamaso pa Mulungu.