Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+

  • Deuteronomo 26:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndipo lero Yehova wakuchititsani kunena kuti mudzakhala anthu ake, chuma chapadera,+ monga mmene anakulonjezerani,+ ndiponso kuti mudzasunga malamulo ake onse,

  • Deuteronomo 32:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pakuti gawo la Yehova ndilo anthu ake.+

      Yakobo ndiye gawo la cholowa chake.+

  • 2 Samueli 20:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ine ndikuimira anthu ofuna mtendere+ ndi okhulupirika+ a mu Isiraeli. Iwe ukufuna kupha mzinda+ ndi mayi mu Isiraeli. N’chifukwa chiyani ukufuna kuwononga+ cholowa+ cha Yehova?”

  • Salimo 135:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ya wadzisankhira Yakobo,+

      Wadzisankhira Isiraeli kukhala chuma chake chapadera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena