Salimo 119:161 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 161 Akalonga amandizunza+ popanda chifukwa,Koma mtima wanga umaopa mawu anu.+