Salimo 119:161 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 161 Akalonga andizunza popanda chifukwa,+Koma mtima wanga umaopa mawu anu.+