Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 19:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kuopa+ Yehova n’koyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya.

      Zigamulo+ za Yehova n’zolondola,+ ndipo pa mbali iliyonse zasonyezadi kuti ndi zolungama.+

  • Miyambo 28:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Wodala ndi munthu amene amaopa Mulungu nthawi zonse,+ koma woumitsa mtima wake adzagwera m’tsoka.+

  • Afilipi 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero, okondedwa anga, monga mmene mwakhalira omvera nthawi zonse,+ osati pokhapokha ine ndikakhalapo,* koma mofunitsitsa kwambiri tsopano pamene ine kulibe, pitirizani kukonza chipulumutso chanu, mwamantha+ ndi kunjenjemera.

  • Aheberi 12:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndiye chifukwa chake, poona kuti tidzalandira ufumu umene sungagwedezeke,+ tiyeni tipitirize kulandira kukoma mtima kwakukulu, kuti kudzera m’kukoma mtima kwakukulu kumeneko, tichitire Mulungu utumiki wopatulika m’njira yovomerezeka, ndipo tiuchite moopa Mulungu komanso mwaulemu waukulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena