Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tumikirani Yehova mwamantha.+

      Kondwerani ndipo nthunthumirani.+

  • Miyambo 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+

  • Miyambo 23:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mtima wako usamasirire anthu ochimwa,+ koma iwe uziopa Yehova tsiku lonse.+

  • Yeremiya 32:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale+ lakuti sindidzasiya kuwachitira zabwino+ ndipo ndidzawapatsa mtima woti azindiopa kuti asachoke kwa ine.+

  • Afilipi 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero, okondedwa anga, monga mmene mwakhalira omvera nthawi zonse,+ osati pokhapokha ine ndikakhalapo,* koma mofunitsitsa kwambiri tsopano pamene ine kulibe, pitirizani kukonza chipulumutso chanu, mwamantha+ ndi kunjenjemera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena