Salimo 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Usapse mtima chifukwa cha anthu ochita zoipa.+Usakhumbe kukhala ngati anthu ochita zosalungama.+ Miyambo 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Usasirire munthu wachiwawa,+ kapena kusankha njira zake.+ Miyambo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usamasirire anthu oipa,+ ndipo usamasonyeze kuti ukusirira kukhala pagulu lawo,+