-
Malaki 2:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Pangano limene ndinachita naye linali loti ndinamupatsa moyo ndi mtendere kuti azindiopa. Iye ankandiopa ndipo ankalemekeza dzina langa.
-