Malaki 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pangano limene ndinapangana naye linasunga moyo wake. Linamuthandizanso kukhala ndi moyo wamtendere.+ Chifukwa cha madalitso amenewa, anali kundiopa.+ Popeza kuti anali kulemekeza dzina langa, sankachita chilichonse chondikwiyitsa.+
5 “Pangano limene ndinapangana naye linasunga moyo wake. Linamuthandizanso kukhala ndi moyo wamtendere.+ Chifukwa cha madalitso amenewa, anali kundiopa.+ Popeza kuti anali kulemekeza dzina langa, sankachita chilichonse chondikwiyitsa.+