Yeremiya 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi upitiriza kulamulira chifukwa chakuti matabwa a mkungudzawa akukuchititsa kukhala wapamwamba kuposa ena? Kodi bambo ako sanali kudya, kumwa ndi kuchita zinthu motsatira malamulo komanso mwachilungamo?+ Chifukwa chochita zimenezi zinthu zinawayendera bwino.+ Mika 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+ Zekariya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Muzichita chilungamo chenicheni poweruza milandu.+ Muzisonyezana kukoma mtima kosatha+ ndi chifundo.+
15 Kodi upitiriza kulamulira chifukwa chakuti matabwa a mkungudzawa akukuchititsa kukhala wapamwamba kuposa ena? Kodi bambo ako sanali kudya, kumwa ndi kuchita zinthu motsatira malamulo komanso mwachilungamo?+ Chifukwa chochita zimenezi zinthu zinawayendera bwino.+
8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+
9 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Muzichita chilungamo chenicheni poweruza milandu.+ Muzisonyezana kukoma mtima kosatha+ ndi chifundo.+