Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Muzisunga malangizo+ ndi zigamulo zake zimene ndikukulamulani lero. Muzitero kuti nthawi zonse zinthu zikuyendereni bwino,+ inuyo ndi ana anu obwera pambuyo panu, ndiponso kuti mutalikitse masiku anu panthaka imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.”+

  • Salimo 128:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Pakuti udzadya zipatso za ntchito ya manja ako.+

      Udzakhala wodala ndipo zinthu zidzakuyendera bwino.+

  • Yesaya 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+

  • Yeremiya 42:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kaya mawu a Yehova Mulungu wathu ndi otikomera kapena otiipira, ife tidzamvera mawuwo. Tidzatero kuti zinthu zitiyendere bwino chifukwa chomvera mawu a Yehova Mulungu wathu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena