Salimo 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova andibwezere mogwirizana ndi chilungamo changa,+Andibwezere mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga pamaso pake.+ Salimo 128:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 128 Wodala ndi aliyense woopa Yehova,+Amene amayenda m’njira za Mulungu.+ Mlaliki 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale woipa atachita zoipa+ maulendo 100 n’kukhala ndi moyo wautali akuchitabe zofuna zake, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino,+ chifukwa chakuti anali kumuopa.+ Zefaniya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+ Aroma 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma aliyense wochita zabwino,+ choyamba Myuda+ kenako Mgiriki,+ adzalandira ulemerero, ulemu ndi mtendere.
24 Yehova andibwezere mogwirizana ndi chilungamo changa,+Andibwezere mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga pamaso pake.+
12 Ngakhale woipa atachita zoipa+ maulendo 100 n’kukhala ndi moyo wautali akuchitabe zofuna zake, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino,+ chifukwa chakuti anali kumuopa.+
3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+
10 Koma aliyense wochita zabwino,+ choyamba Myuda+ kenako Mgiriki,+ adzalandira ulemerero, ulemu ndi mtendere.