Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 6:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+

  • Aroma 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mu uthenga wabwinowu, chilungamo+ cha Mulungu chimaululidwa chifukwa cha chikhulupiriro cha munthu.+ Zikatero, chikhulupiriro cha munthuyo chimalimbanso monga mmene Malemba amanenera kuti: “Koma wolungama adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.”+

  • Aroma 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndipo posadziwa chilungamo cha Mulungu,+ iwo sanagonjere chilungamocho+ koma anayesetsa kukhazikitsa chawochawo.+

  • Aefeso 4:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 ndi kuvala+ umunthu watsopano+ umene unalengedwa+ mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndipo umatsatira zofunika pa chilungamo chenicheni+ ndi pa kukhulupirika.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena