Yohane 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Iye wokhulupirira+ mwa Mwanayo ali nawo moyo wosatha.+ Wosamvera Mwanayo sadzauona moyowu,+ koma mkwiyo wa Mulungu ukhalabe pa iye.+ Afilipi 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiponso kuti ndikapezeke wogwirizana ndi iye ndikuchita chilungamo. Osati chilungamo changachanga chobwera ndi chilamulo,+ koma chobwera mwa kukhulupirira+ Khristu, chochokera kwa Mulungu pa maziko a chikhulupiriro.+
36 Iye wokhulupirira+ mwa Mwanayo ali nawo moyo wosatha.+ Wosamvera Mwanayo sadzauona moyowu,+ koma mkwiyo wa Mulungu ukhalabe pa iye.+
9 Ndiponso kuti ndikapezeke wogwirizana ndi iye ndikuchita chilungamo. Osati chilungamo changachanga chobwera ndi chilamulo,+ koma chobwera mwa kukhulupirira+ Khristu, chochokera kwa Mulungu pa maziko a chikhulupiriro.+