Aroma 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma adzapereka chilango ndi mkwiyo+ kwa okonda mikangano+ amenenso samvera choonadi+ koma amamvera zosalungama. Aefeso 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu asakupusitseni ndi mawu opanda pake,+ pakuti mkwiyo wa Mulungu udzafika pa ana a kusamvera, ochita zinthu zimene ndatchulazi.+ Aheberi 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma pali chiyembekezo china choopsa cha chiweruzo,+ ndiponso pali nsanje yoyaka moto imene idzawononge otsutsawo.+
8 Koma adzapereka chilango ndi mkwiyo+ kwa okonda mikangano+ amenenso samvera choonadi+ koma amamvera zosalungama.
6 Munthu asakupusitseni ndi mawu opanda pake,+ pakuti mkwiyo wa Mulungu udzafika pa ana a kusamvera, ochita zinthu zimene ndatchulazi.+
27 Koma pali chiyembekezo china choopsa cha chiweruzo,+ ndiponso pali nsanje yoyaka moto imene idzawononge otsutsawo.+