Yesaya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa anthu oipa! Iwo adzaona zoopsa, chifukwa zimene anachitira ena ndi manja awo, zidzawachitikira iwowo.+ Aroma 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mkwiyo wa Mulungu+ ukusonyezedwa kuchokera kumwamba pa anthu onse osaopa Mulungu ndi ochita zosalungama+ amene akupondereza choonadi+ m’njira yosalungama.+ Akolose 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa cha zinthu zimenezi, mkwiyo wa Mulungu ukubwera.+ Aheberi 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma pali chiyembekezo china choopsa cha chiweruzo,+ ndiponso pali nsanje yoyaka moto imene idzawononge otsutsawo.+
11 Tsoka kwa anthu oipa! Iwo adzaona zoopsa, chifukwa zimene anachitira ena ndi manja awo, zidzawachitikira iwowo.+
18 Mkwiyo wa Mulungu+ ukusonyezedwa kuchokera kumwamba pa anthu onse osaopa Mulungu ndi ochita zosalungama+ amene akupondereza choonadi+ m’njira yosalungama.+
27 Koma pali chiyembekezo china choopsa cha chiweruzo,+ ndiponso pali nsanje yoyaka moto imene idzawononge otsutsawo.+