Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Munthu amene sadalira ntchito zake koma amakhulupirira+ Mulungu, amayesedwa wolungama chifukwa cha chikhulupiriro chake,+ pakuti Mulungu amatha kuona munthu wosatsatira malamulo ake kukhala wolungama.

  • Aroma 9:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndiye tinene kuti chiyani? Tinene kuti, ngakhale kuti anthu a mitundu ina sanatsatire chilungamo, iwo anapeza chilungamo+ chimene chimapezeka chifukwa cha chikhulupiriro.+

  • Agalatiya 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Popeza tikudziwa kuti munthu amayesedwa wolungama+ mwa kukhulupirira+ Khristu Yesu, osati chifukwa cha ntchito za chilamulo, ife takhulupirira Khristu Yesu. Tachita zimenezi kuti tiyesedwe olungama chifukwa cha chikhulupiriro chathu mwa Khristu,+ osati mwa ntchito zotsatira chilamulo. Tatero chifukwa palibe munthu adzayesedwa wolungama chifukwa cha ntchito zotsatira chilamulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena