Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ngati chifukwa cha uchimo wa munthu mmodziyo+ imfa inalamulira monga mfumu+ kudzera mwa munthuyo, amene alandira kukoma mtima kwakukulu+ kochuluka ndiponso mphatso yaulere+ yaikuluyo ya chilungamo, adzakhala ndi moyo ndi kulamulira monga mafumu+ kudzera mwa munthu mmodziyu, Yesu Khristu.+

  • 1 Akorinto 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndipo ena mwa inu munali otero.+ Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mwayesedwa olungama+ m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu,+ komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.+

  • Aheberi 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pakuti Chilamulo sichinapangitse chilichonse kukhala changwiro,+ koma chiyembekezo+ chabwino kwambiri chimene anabweretsa kuwonjezera pa Chilamulocho, chinachita zimenezo. Ife tikuyandikira kwa Mulungu chifukwa cha chiyembekezo chimenecho.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena