Aheberi 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chilamulo sichinapangitse chilichonse kukhala changwiro.+ Koma chiyembekezo cha zinthu zabwino chimene anabweretsa,+ chomwe chikutithandiza kuyandikira Mulungu,+ chinachita zimenezi. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2023, tsa. 25
19 Chilamulo sichinapangitse chilichonse kukhala changwiro.+ Koma chiyembekezo cha zinthu zabwino chimene anabweretsa,+ chomwe chikutithandiza kuyandikira Mulungu,+ chinachita zimenezi.